Ezekiel 48:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Dani, kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Asere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi m'malire a Dani, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Asere, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Aseri adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi dziko la Dani kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi m'malire a Dani, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Aseri, limodzi.