Ezekiel 48:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chigawo cha Alevi ndi chigawo cha mzinda zikhale pakati pa dera la mfumulo. Dera limenelo lidzakhale pakatimpakati pa dziko la Yuda ndi la Benjamini.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuyambira tsono dziko la Alevi kufikira dziko la mudzi, ndiwo a pakati pa magawo ake a kalonga, pakati pa malire a Yuda ndi malire a Benjamini, kukhale kwa kalonga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho chigawo cha Alevi ndi chigawo cha mzinda zidzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzayambira mbali ya kummawa mpaka ya kumadzulo kwa dziko la Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuyambira tsono dziko la Alevi kufikira dziko la mudzi, ndiwo a pakati pa magawo ace a kalonga, pakati pa malire a Yuda ndi malire a Benjamini, kukhale kwa kalonga.