Ezekiel 48:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Za mafuko ena otsala zidzayenda motere: kuyambira kuvuma mpaka kuzambwe padzakhala chigawo chimodzi, chimenechi ncha Benjamini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za mafuko otsala tsono, kuyambira kumbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo, Benjamini akhale nalo gawo limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Za mafuko ena otsala zidzayenda motere: Benjamini adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzayambira mbali ya kummawa mpaka ya kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za mafuko otsala tsono, kuyambira ku mbali ya kum'mawa kufikita mbali ya kumadzulo, Benjamini akhale nalo gawo limodzi.