Ezekiel 48:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Simeoni, kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Isakara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kumalire a Simeoni kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Isakara, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Isakara adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi chigawo cha Simeoni kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku malire a Simeoni kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Isakara, limodzi.