Ezekiel 48:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Isakara, kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Zebuloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kumalire a Isakara, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Zebuloni, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Zebuloni adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi chigawo cha Isakara kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku malire a Isakara, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Zebuloni, limodzi.