Ezekiel 48:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Zebuloni, kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Gadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kumalire a Zebuloni, kuyambira kumbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Gadi, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Gadi adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi chigawo cha Zebuloni kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku malire a Zebuloni, kuyambira ku mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Gadi, limodzi.