Ezekiel 48:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malire a Gadi mbali yakumwera ku Negebu achokere kumwera kuyambira ku Tamara mpaka ku Dziŵe la Meriboti-Kadesi, kenaka kuchokera ku Mtsinje wa ku Ejipito, kukafika ku Nyanja Yaikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ku malire a Gadi, mbali ya kumwera, kuloza kumwera, malire akhale kuyambira ku Tamara kufikira ku madzi a Meribati-Kadesi, ku mtsinje wa Ejipito, kufikira ku Nyanja Yaikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Malire a Gadi a mbali yakummwera ku Negevi adzayenda kuchokera ku Tamara mpaka ku dziwe la Meriba Kadesi komanso kuchokera ku Mtsinje wa Igupto mpaka ku Nyanja Yayikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku malire a Gadi, mbali ya kumwela, kuloza kumwela, malire akhale kuyambira ku Tamara kufikira ku madzi a Meribati ndi Kadesi, ku mtsinje wa Aigupto, kufikira ku nyanja yaikuru.