Ezekiel 48:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kukhale zipata zitatu: chipata cha Rubeni, cha Yuda, ndi cha Levi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zipata za mudzi zidzakhala monga mwa maina a mafuko a Israele; zipata zitatu kumpoto: chipata chimodzi cha Rubeni, chipata chimodzi cha Yuda, chipata chimodzi cha Levi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kudzakhale zipata zitatu izi: cha Rubeni, cha Yuda ndi cha Levi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zipata za mudzi zidzakhala monga mwa maina a mafuko a Israyeli; zipata zitatu kumpoto: cipata cimodzi ca Rubeni, cipata cimodzi ca Yuda, cipata cimodzi ca Levi;