Ezekiel 48:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuvuma, kumene kutalika kwake ndi kwa mamita 2,250, kukhale zipata zitatu: chipata cha Yosefe, cha Benjamini ndi cha Dani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ku mbali ya kum'mawa zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zitatu: chipata chimodzi cha Yosefe, chipata chimodzi cha Benjamini, chipata chimodzi cha Dani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mbali ya kummawa, imene kutalika kwake ndi mamita 2,250, kudzakhala zipata zitatu izi: chipata cha Yosefe, chipata cha Benjamini ndi chipata cha Dani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ku mbali ya kum'mawa zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zitatu: cipata cimodzi ca Yosefe, cipata cimodzi ca Benjamini, cipata cimodzi ca Dani;