Ezekiel 48:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuzambwe, kumene kutalika kwake ndi kwa mamita 2,250, kukhale zipata zitatu: chipata cha Gadi, cha Asere ndi cha Nafutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kumbali ya kumadzulo mikono zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zake zitatu: chipata cha Gadi, chipata chimodzi cha Asere, chipata chimodzi cha Nafutali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mbali ya kumadzulo, imene kutalika kwake ndi mamita 2,250 kudzakhala zipata zitatu izi: chipata cha Gadi, chipata cha Aseri ndi chipata cha Nafutali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ku mbali ya kumadzulo zikwi zinai mphambu mazana asanu, ndi zipata zace zitaru; cipata cimodzi ca Gadi, cipata cimodzi ca Aseri, cipata cimodzi ca Nafitali.