Ezekiel 48:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Nafutali kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi m'malire a Nafutali, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Manase, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Manase adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi dziko la Nafutali kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi m'malire a Nafitali, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Manase, limodzi.