Ezekiel 48:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchitana malire ndi Efuremu kuchokera kuvuma mpaka kuzambwe, padzakhala chigawo cha Rubeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi m'malire a Efuremu, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Rubeni, limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Rubeni adzakhala ndi chigawo chimodzi. Chidzachita malire ndi Efereimu kuchokera kummawa mpaka kumadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi m'malire a Efraimu, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Rubeni, limodzi.