Ezekiel 5:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe Yerusalemu, ndidzakusandutsa bwinja. Udzakhala chinthu chonyozeka m'maso mwa anthu a mitundu yokuzungulira ndi kwa onse odutsapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakuikanso ukhale bwinja ndi chotonza pakati pa amitundu akukuzinga, pamaso pa onse akupitirirapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndidzakusandutsa iwe bwinja ndi chinthu chonyozeka pakati pa anthu a mitundu ina amene akuzungulira, ndi kwa onse odutsapo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuikanso ukhale bwinja ndi cotonza pakati pa amitundu akukuzinga, pamaso pa onse akupitirirapo.