Ezekiel 6:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo adzadziŵa kuti Ine ndine Chauta, ndipo sindinkaŵaopseza chabe pamene ndinkanena kuti ndidzaŵalanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, sindinanena chabe kuti ndidzawachitira choipa ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iwo adzadziwa kuti ndine Yehova ndi kuti sindinkawaopseza chabe pamene ndinanena kuti ndidzawawononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, sindinanena cabe kuti ndidzawacitira coipa ici.