Ezekiel 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, uyang'ane ku mapiri a ku Israele, ndipo uŵadzudzule ndi mau aŵa akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako kumapiri a Israele, uwanenere,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, yangʼana ku mapiri a Israeli; yankhula nawo modzudzula
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku mapiri a Israyeli, uwanenere,