Ezekiel 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mitembo ya Aisraele ndidzaimwaza patsogolo pa mafano ao. Ndidzamwaza mafupa anu pozungulira maguwa anu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzaika mitembo ya ana a Israele pamaso pa mafano anu, ndi kumwaza mafupa anu mozungulira maguwa anu a nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzagoneka mitembo ya Aisraeli pamaso pa mafano awo, ndipo ndidzamwaza mafupa anu mozungulira maguwa anu ansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzaika mitembo ya ana a Israyeli pamaso pa mafano anu, ndi kumwaza mafupa anu mozungulira maguwa anu a nsembe.