Ezekiel 6:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu anu adzaphedwa pakati panu, motero mudzadziŵa kuti Ine ndine Chauta.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ophedwa adzagwa pakati panu, motero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu anu adzaphedwa pakati panu, ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ophedwa adzagwa pakati panu, matero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.