Ezekiel 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwuzanso kuti, “Udzaŵaonanso akuchita zonyansa zina zazikulu kupambana zimenezi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatinso kwa ine, Udzaonanso zonyansa zazikulu zina azichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anandiwuzanso kuti, ‘Iwe udzawaonanso akuchita zinthu zonyansa kwambiri.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatinso kwa ine, Udzaonanso zonyansa zazikuru zina azicita.