Ezekiel 8:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ulemerero wa Mulungu wa Israele udaoneka kumeneko, monga momwe ndidaaonera kale m'masomphenya m'chigwa muja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo taonani, pomwepo panali ulemerero wa Mulungu wa Israele, monga mwa maonekedwe ndinawaona kuchidikha chija.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumeneko ndinaona ulemerero wa Mulungu wa Israeli ngati momwe ndinaonera mʼmasomphenya mʼchigwa muja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo taonani, pomwepo panali ulemerero wa Mulungu wa lsrayeli, monga mwa maonekedwe ndinawaona ku cidikha cija.