Ezekiel 8:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adapita nane ku khomo loloŵera ku bwalo la Nyumba ya Mulungu. Ine poyang'ana, ndidaona dzenje pakhomapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza nane kuchipata cha kubwalo, ndipo popenya ine, taonani, pobooka palinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Iye anandipititsa ku khomo lolowera ku bwalo la Nyumba ya Mulungu. Nditayangʼanitsitsa ndinangoona dzenje pa khomapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza nane ku cipata ca kubwalo, ndipo popenya ine, taonani, pobooka palinga.