Ezekiel 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandiwuza kuti, “Loŵa, uwone zonyansa zazikulu zimene anthu akuchita kuno.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Lowa, kapenye zonyansa zoipa alikuzichita komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anandiwuza kuti, “Lowa, ndipo ona zinthu zonyansa zimene akuchita pamenepa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Lowa, kapenye zonyansa zoipa alikuzicita komweko.