Ezekiel 9:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka ndidamva Mulungu akuuza anzake ena aja kuti, “Mtsateni mumzinda monse, mukakanthe aliyense. Musakachite kaso ndi aliyense, musakachite konse chifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa enawo, ndilikumva ine, Pitani pakati pa mudzi kumtsata iye, ndi kukantha; maso anu asalekerere, musachite chifundo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ndinamva Yehova akuwuza anthu ena aja kuti, “Mutsateni mu mzinda wonse ndipo mukakanthe aliyense mopanda kumvera chisoni kapena chifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa enawo, nditikumva ine, Pitani pakati pa mudzi kumtsata iye, ndi kukantha; maso anu asalekerere, musacite cifundo;