Ezekiel 9:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adanena kuti, “Iipitseni Nyumba yangayo, ndipo mabwalo ake muŵadzaze ndi mitembo. Tiyeni, pitani!” Motero iwo adapita kukapha anthu mumzindamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa iwo, Muipse nyumbayi ndi kudzaza mabwalo ndi ophedwa, mukani. Ndipo anatuluka, nakantha m'mudzimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anawawuza kuti, “Ipitsani Nyumba ya Mulungu ndipo mudzaze mabwalo ake ndi anthu akufa. Pitani.” Choncho iwo anapita nayamba kupha anthu mu mzinda monse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa iwo, Muipse nyumbayi ndi kudzaza mabwalo ndi ophedwa, mukani. Ndipo anaturuka, nakantha m'mudzimo.