Ezra 10:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lapani tsopano kwa Chauta, Mulungu wa makolo anu, ndipo muchite zimene Iye akufuna. Dzichotseni pakati pa mitundu ya anthu a m'maiko enaŵa, ndi pa akazi achilendowo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tsono, wululani kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, nimuchite chomkondweretsa; mudzilekanitse ndi mitundu ya anthu a m'dzikomo, ndi kwa akazi achilendo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano lapani kwa Yehova, Mulungu wa makolo anu ndi kuchita zimene akufuna. Dzipatuleni kwa anthu a mayiko enawa ndi kwa akazi achikunjawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tsono, ululani kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, nimucite comkondweretsa; mudzilekanitse ndi mitundu ya anthu a m'dzikomo, ndi kwa akazi acilendo.