Ezra 10:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chitamva mau amenewo, chinantindi chonse chapamsonkhanopo chidayankha mokweza mau kuti, “Ndi chonchodi, tiyenera kuchitadi monga mwaneneramo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo unayankha msonkhano wonse, ndi kunena ndi mau akulu, Monga mwa mau anu tiyenera kuchita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu lonse la anthu linayankha ndi mawu ofuwula kuti, “Nʼzoona! Tichita monga mwaneneramu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo unayankha msonkhano wonse, ndi kunena ndi mau akuru, Monga mwa mau anu tiyenera kucita.