Ezra 10:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yonatani yekha, mwana wa Asahele, ndiponso Yahazeiya, mwana wa Tikiwa, ndi amene adatsutsapo pa zimenezi, ndipo Mesulamu pamodzi ndi Mlevi Sabetai, adaŵavomereza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yonatani mwana wa Asahele ndi Yazeya mwana wa Tikiva okha anatsutsana nacho, ndi Mesulamu ndi Sabetai Mlevi anawathandiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yonatani yekha mwana wa Asaheli ndi Yahazieli mwana wa Tikiva ndiwo anatsutsapo pa zimenezi. Tsono Mesulamu ndi Mlevi Sebetai anawayikira kumbuyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yonatani mwana wa Asaheli ndi Yazeya mwana wa Tikiva okha anatsutsana naco, ndi Mesulamu ndi Sabetai Mlevi anawathandiza.