Ezra 10:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, anali atathana nawo anthu amene adaakwatira akazi achilendo aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natsiriza nao amuna onse adadzitengera akazi achilendo tsiku loyamba la mwezi woyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pofika tsiku loyamba la mwezi woyamba anali atathana nawo anthu amene anakwatira akazi achilendo aja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natsiriza nao amuna onse adadzitengera akazi acilendo tsiku loyamba la mwezi woyamba.