Ezra 10:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pa Israele: a fuko la Parosi anali Ramiya, Iziya, Malikiya, Miyamini, Eleazara, Hasabiya ndi Benaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Aisraele a ana a Parosi: Ramiya, ndi Iziya, ndi Matikiya, ndi Miyamini, ndi Eleazara, ndi Malikiya, ndi Benaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ochokera pakati pa Aisraeli ena: a fuko la Parosi anali Ramiya, Iziya, Malikiya, Miyamini, Eliezara, ndi Benaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Aisrayeli a ana a Parosi: Ramiya, ndi Iziya, ndi Matikiya, ndi Miyamini, ndi Eleazara, ndi Malikiya, ndi Benaya.