Ezra 10:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Bebai anali Yehohanani, Hananiya, Zabibai ndi Atilai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Bebai: Yehohanani, Hananiya, Zabai, Atilai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
A fuko la Bebai anali Yehohanani, Hananiya, Zabayi ndi Atilayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Bebai: Yehohanana, Hananiya, Zabai, Atilai.