Ezra 10:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Pahatimowabu anali Adina, Kelali, Benaya, Maaseiya, Mataniya, Bezalele, Binuyi ndi Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Pahatimowabu: Adina, ndi Kelali, Benaya, Maaseiya, Mataniya, Bezalele, ndi Binuyi, ndi Manase.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
A fuko la Pahati-Mowabu anali Adina, Kelali, Benaya, Maseya, Mataniya, Bezaleli, Binuyi ndi Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Pahati: Moabu, Adina, ndi Kelali, Benaya, Maseya, Mataniya, Bezaleli, ndi Binui, ndi Manase.