Ezra 10:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onseŵa adaakwatira akazi achilendo. Tsono adaŵasudzula akaziwo pamodzi ndi ana ao omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Awa onse adatenga akazi achilendo, ndi ena a iwowa anali ndi akazi amene adawabalira ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onsewa anakwatira akazi achilendo. Tsono anawasudzula akaziwo ndi kuwatumiza kwawo pamodzi ndi ana awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Awa onse adatenga akazi acilendo, ndi ena a iwowa anali ndi akazi amene adawabalira ana.