Ezra 2:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Azigadi, 1,222.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Azigadi, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi awiri ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zidzukulu za Azigadi — 1,222
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Asigadi, cikwi cimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi awiri ndi awiri.