Ezra 2:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Rama ndi Geba, 621.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Rama ndi Geba, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu aamuna a ku Rama ndi Geba — 621
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Rama ndi Gaba, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza mmodzi.