Ezra 2:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amuna a ku Betele ndi ku Ai, 223.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu a ku Betele ndi Ai, mazana awiri mphambu makumi awiri kudza atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu aamuna a ku Beteli ndi Ai — 223
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu a ku Beteli ndi Ai, mazana awiri mphambu makumi awiri kudza atatu.