Ezra 2:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Elamu wina, 1,254.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Elamu wina, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu aamuna a ku Elamu wina — 1,254
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Elamu wina, cikwi cimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.