Ezra 2:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Sena, 3,630.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Senaa, zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi kudza makumi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu aamuna a ku Sena — 3,630.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Senai, zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi kudza makumi atatu.