Ezra 2:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Pasuri, 1,247.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Pasuri — 1,247
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Pasuru, cikwi cimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.