Ezra 2:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alevi anali aŵa: a banja la Yesuwa ndi la Kadimiyele, ndiye kuti zidzukulu za Hodaviya, 74.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alevi: ana a Yesuwa, ndi Kadimiyele, ndiwo a ana a Hodaviya, makumi asanu ndi awiri mphambu anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alevi anali awa: Zidzukulu za Yesuwa ndi Kadimieli (kudzera mwa ana a Hodaviya) — 74.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alevi: ana a Yesuwa, ndi Kadimiyeli, ndiwo a ana a Hodariya, makumi asanu ndi awiri mphambu anai.