Ezra 2:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Oimba nyimbo anali aŵa: a banja la Asafu, 128.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oimba: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu oyimba nyimbo anali awa: Zidzukulu za Asafu — 128.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oyimba: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.