Ezra 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Pahatimowabu, ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa ndi Yowabu, 2,812.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zidzukulu za Pahati-Mowabu (zochokera kwa Yesuwa ndi Yowabu) — 2,812
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Pahati Moabu, a ana a Yesuwa ndi Yoabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi awiri.