Ezra 2:67 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngamira zao zinalipo 435 ndipo abulu ao analipo 6,720.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu; abulu zikwi zisanu ndi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngamira 435 ndi abulu 6,720.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu; aburu zikwi zisanu ndi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.