Ezra 2:69 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapereka kwa msungachuma wa ntchitoyo molingana ndi chuma chao, golide wa makilogaramu 500, ndi siliva wa makilogaramu 2,800, ndiponso zovala za ansembe zokwanira 100.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga momwe anakhoza anapereka kuchuma cha ntchitoyi madariki agolide zikwi zisanu ndi chimodzi, miyeso ya mina ya siliva zikwi zisanu, ndi malaya a ansembe zana limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapereka kwa msungichuma wa ntchitoyo molingana ndi mmene aliyense chuma chake chinalili: golide wa makilogalamu 500, siliva makilogalamu 2,800 ndi zovala za ansembe zokwanira 100.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga momwe anakhoza anapereka ku cuma ca nchitoyi madariki agolidi: zikwi zisanu ndi cimodzi, miyeso ya siliva zikwi zisanu, ndi maraya a ansembe zana limodzi.