Ezra 3:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mwezi wachisanu ndi chiŵiri, ana a Aisraele ali m'midzi mwao, anthu adasonkhana ku Yerusalemu ndi cholinga chimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Utakhala tsono mwezi wachisanu ndi chiwiri, ana a Israele ali m'midzimo, anthuwo anasonkhana ngati munthu mmodzi ku Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Utafika mwezi wa chisanu ndi chiwiri Aisraeli atakhala kale mʼmidzi yawo, anthu anasonkhana ku Yerusalemu ndi cholinga chimodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Utakhala tsono mwezi wacisanu ndi ciwiri, ana a Israyeli ali m'midzimo, anthuwo anasonkhana ngati munthu mmodzi ku Yerusalemu.