Ezra 3:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake ankapereka nsembe zopsereza monga mwa nthaŵi zonse, nsembe zopereka pokhala mwezi ndi pa masiku onse achikondwerero oikidwa otamandira Chauta, kudzanso nsembe zaufulu zopereka kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
atatero anaperekanso nsembe yopsereza yosalekeza, ndi za pokhala mwezi, ndi za nyengo zoikika zonse za Yehova zopatulika, ndi za munthu yense wopereka nsembe yaufulu kwa Yehova mwaufulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake, ankapereka nsembe zopsereza, nsembe zopereka pa nthawi ya mwezi watsopano ndi za pa masiku onse a chikondwerero oyikidwa kutamandira Yehova, kudzanso nsembe zaufulu zopereka kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
atatero anaperekanso nsembe yopsereza yosalekeza, ndi za pokhala mwezi, ndi za nyengo zoikika zonse za Yehova zopatulika, ndi za munthu yense wopereka nsembe yaufulu kwa Yehova mwaufulu.