Ezra 4:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani a Yuda ndi a Benjamini adaamva kuti anthu obwerako ku ukapolo aja akumangira Nyumba Chauta, Mulungu wa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atamva tsono adani a Yuda ndi Benjamini kuti ana aja a ndende analikumangira Yehova Mulungu wa Israele Kachisi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani a Yuda ndi Benjamini anamva kuti anthu obwera ku ukapolo aja akumangira Nyumba Yehova, Mulungu wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atamva tsono a adani Yuda ndi Benjamini kuti ana aja a ndende analikumangira Yehova Mulungu wa Israyeli Kacisi,