Ezra 4:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ntchito yomanga Nyumba ya Mulungu ku Yerusalemu idalekeka mpaka chaka chachiŵiri cha ufumu wa Dariusi, mfumu ya ku Persiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo inalekeka ntchito ya nyumba ya Mulungu yokhala ku Yerusalemu; nilekeka mpaka chaka chachiwiri cha ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero ntchito yomanga Nyumba ya Mulungu ku Yerusalemu inayimitsidwa mpaka chaka cha chiwiri cha ulamuliro wa Dariyo mfumu ya ku Perisiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo inalekeka nchito ya nyumba ya Mulungu yokhala ku Yerusalemu; nilekeka mpaka caka caciwiri ca ufumu wa Dariyo mfumu ya Perisiya.