Ezra 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalemba akuluakulu ena kuti alepheretse cholinga chao cha pa ntchitoyo pa nthaŵi yonse ya Kirusi, mfumu ya ku Persiya, ngakhalenso mpaka pamene Dariusi, mfumu ya ku Persiya ankalamulira dzikolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nalembera opangira atsutsane nao, nafafanize uphungu wao, masiku onse a Kirusi mfumu ya Persiya, mpaka ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Analemba alangizi ena kuti alepheretse cholinga chawo pa ntchitoyo pa nthawi yonse ya Koresi, mfumu ya ku Perisiya, ndiponso mpaka pamene Dariyo mfumu ya ku Perisiya ankalamulira dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nalembera opangira atsutsane nao, nafafanize uphungu wao, masiku onse a Koresi mfumu ya Perisiya, mpaka ufumu wa Dariyo mfumu ya Perisiya.