Ezra 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mfumu Ahasuwero adayamba kulamulira dziko, adani aja adalemba kalata yoneneza nzika zija za ku Yuda ndi za ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pokhala mfumu Ahasuwero, poyambira ufumu wake, analembera chowaneneza okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Ahasiwero atangoyamba kulamulira dzikolo, adani aja analemba kalata yoneneza anthu a Yuda ndi Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pokhala mfumu Ahaswero, poyambira ufumu wace, analembera cowaneneza okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu.