Ezra 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kalatayi ikuchokera kwa Rehumu bwanamkubwa, mlembi Simisai ndi anzao aŵa: aweruzi, nduna ndi akuluakulu ena, anthu a ku Persiya ndi ku Ereki, ku Babiloniya, ndi ku Susa, m'dziko la Elami.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nalembera Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi Simisai mlembi, ndi anzake otsala; Adinai, ndi Afarisatikai, Ataripilai, Afarisai, Aereke, Ababiloni, Asusani, Adehai, Aelamu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kalata yochokera kwa Rehumu, mkulu wa gulu lankhondo, mlembi Simisai ndi anzawo awa: oweruza, nduna, akuluakulu ena, anthu a ku Peresiya, Ereki, Babuloni, Susa mʼdziko la Elamu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nalembera Rehumu ciwinda ca malamulo, ndi Simsai mlembi, ndi anzace otsala; Adinai, ndi Afarisatikai, Ataripilai, Afarisai, Arekavai, Ababulo, Asusanekai, Adehai, Aelimai,