Ezra 5:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo aneneri aŵa, Hagai ndi Zekariya mwana wa Ido, adayamba kulankhula kwa Ayuda okhala m'dziko la Yuda ndi mu Yerusalemu. Ankalankhula m'dzina la Mulungu wa Israele amene anali nawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo aneneri, Hagai mneneriyo, ndi Zekariya mwana wa Ido, ananenera kwa Ayuda okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu; m'dzina la Mulungu wa Israele ananenera kwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyo aneneri Hagai ndi Zekariya, mwana wa Ido, ankayankhula kwa Ayuda okhala mʼdziko la Yuda ndi mu Yerusalemu mʼdzina la Mulungu wa Israeli, amene anali nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo aneneri, Hagai mneneriyo, ndi Zekariya mwana wa Ido, ananenera kwa Ayuda okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu; m'dzina la Mulungu wa Israyeli ananenera kwa iwo.